
Pocket WiFi and Smart box Router
Pezani wifi pamtengo wotsika ya speed yodaliraka. Mtengo wa k20,000 yokha mugula pocket wifi ndipo k30,000 Yokha mupeza router Router imapanga connect up to 32 devices Imabwera ndi charge ethenet cable iliso ndi battery limalimba kwa tsiku lose. Pocket WiFi imapanga connect up to 10 devices ili ndi battery.Mumagwiritsa ntchito ku zithu zofuna internet laptop, desktop, CCTV, extreme decoder, smart TV, See more
Price: MWK20
Private Seller: Takwah K