
Car for sale
Dzaodeni daihatsu hijet iyi yakhala almost a year osalizidwako. Ilibe battery, starter motor ikufunika kuigwirako komaso wireling izafunikako, engen ndi gearbox sizinagwiridweko chibweleleni. Mukafuna kuiona mutha kuimba pa number iyi; 0988714258. Ili ku Lilongwe chiwoko
Price: MK800
Private Seller: Charles J