Mwanawanga taona wafaira perfume onunkhira komaso udura mtembo wanga kumachita kuti ndili moyo ndikazola mafuta a mteza kuli kusowa kwa mafuta. Mtembo wanga wauveka zovala zodura kwambiri kumachita kuti pomwe ndili moyo ukalephera ndi kundigulira kutchena/kaunjika amene.… More