Tikhala ndi ma lessons a Hungarian sausage, beef sausage komanso tsp sausage pa mtengo wa K5000 yokha pa 31 July Blantyre ndipo kuzakhalanso lesson ya how to order from China pa mtengo wa 3500. Tiziyenda madela monga mulanje zomba lilongwe nsanje chikwawa ndi ndi mzuzu kuti mudziwe zambiri drop your app numbers to be added to the group
$5,000