- Uku nku area 25 chabe .... NDE Kulinso ku By-pass, chilinde, Lumbadzi, Chiseka nseu wa Bunda, chitedze, NRC, 6miles etc ... Chofunika kuchita inuyo imbileni foni olo watsap me kapena lowani ku watsap group potumiza ADD ku 09916 17453... Chonde chonde musaike nambala yanu pano.. KOMANSO omwe mukugulitsa malo, nyumba, olo munda inbox me kapena lowani ku group ko mukumane nokha ndi ogula/ogulitsa popanda mkhalapakati!
$11