Munda ogulitsa ku nkhotakota T/A kafuzira , malire ndi mzimba,Malowa ndi okwana 16 hector's,Pamalopo Pali nyumba ya Malata 30, dimba lokwana 1 hector , mitengo ya Blue gum yokwana 1 hector , komaso mitengo ya chilengedwe , madzi ndi osavuta pa malopo ku mtsinje wa lupachi madzi samaphwera Chaka chose,Malowa akugulitsolidwa pa mtengo wa 2 million… Ona kwacha kukambirana kulipo
$2