Tili ndi ma farm ogulitsa ku mchinji Kuma T/A AWA, mkanda, mlonyeni, mduwa, dambe, simphasi, nyoka, kazyozo, mavwere, kapondo ndi simphasi,Pamene ku kasungu ndi ma T A AWA, Mnthunduwala, nyaza, santhe, Chaima ndi kawamba,Mtengo ndi k 200,000 per acre , koma timachotsera malingana ndikukula kwa malo amene mungatenge and kalipilidwe kandalama,Imbani kapena wtsup pa 0888426220
FREE