Plot for sale in Blantyre Chisa,in chilobwe township. Malowa Ali mu shape ya trapezium 56,37,24,63 metres. Pali Manyumba atatu. Magesi palibe koma ma neighbors Ali nawo,madzi alipo ndipo ndikosafika galimoto. Oakonda ndiimbileni pa 0991506776,0881567670 or WhatsApp 0996416231. Ndimafunapo 3.4 million kwacha. Koma serious customers tikambilana. Na agent musandiimbile please.
$4