Zomwe mukuonazo ndi zimene mudzazione K570 000 plot payable 10months

-Malowa ali ku airwing after Balon estate.. mwina 18kms from gateway mall. - Omwe mukaika , kuti nzosatheka, ingodutsani, kaguleni ku ma kampani konko...,- kukula kwa malo ndi 15 by 30 meters kapena kuposera apo malinga ndi mthumba mwanu..,-Ofunawo imbani olo watsap me 0991617453.... Kapena lowani ku watsap group

$11

seller's name'
Name: Joel S
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 29 October, 2021

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0991617453

Product Images

product image 0
Image 1 of 1