Tili ndi nyumba komaso Malo ogulitsa m'boma la zomba madela awa, chinamwali, airwing, chilunga/Thom Allan, malonje malile ndi oldnice, Jokala, songani, Naizi, thundu, mtiya ndi madela ena ambiri. Nyumba zikuyambila 2.3million mpaka 80million, Malo akuyambila mk800,000 mpaka 13million..imbani foni pa 0993663970/0881573560 kuti mudziwe zambiri.
FREE