Nditha kutsimikiza kuti panopa atsalapo 15plots Ku Lumbadzi behind blessings

- Mupereke pang'ono pang'ono mpaka miyezi 5 - mtengo ndi k500pin per plot of 15 by 30 meters kapena kuposera apo malinga ndi mthumba mwanu. - Malowa alibe milandu illiyonse.. -Ofunawo imbani olo watsap kapena bwerani ku office ku area 25 B pa Stanley Lodge.... Dziwani kuti tili ndi maploti ndi nyumba zambiri ku area 25, airwing, kaphiri, By-pass, chiseka nseu wa Bunda etc...zogulitsa pangongole ngati inuyo muli achilungamo komanso okhulupilika....

$11

seller's name'
Name: Joel S
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 09 December, 2021

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 2
product image 1
Image 2 of 2