Monga ndanena kale kuti nyumbayi ndatsitsiratu mtengo iliku area 50 lilongwe , nyumbayi ili mphepete mwa mseu wafumbi , pipe ya water board ili pafupinso , size ya plot ndi 15 by 30 meters , ili kufupi ndi double school Chosangalatsa kwambiri pali mwai woti mpanda unamangidwa kale mbali ziwiri ndi aneba Mwai uwu osakuphonyeni Area 50 ndi imodzi mwa ma area alipafupi town komanso madzi ndi magetsi zinafika kale kale İngoyimbani phone yanga :0992335517 , kuti tipanga bussiness tikufuna ndalamazo tikamalizire nyumba
FREE