Malata ogulitsa ndima 32 gauge komaso ndima 12 fit. Malatawo ndi anyuwani mtengo ndi k7900 kukambilana kulipo. Call or WhatsApp pa nambala iyi 0990598080. Ndimapezekera ku lilongwe area 44 Tambalale.
FREE