Manyumba onsewa alipa plot imodzi ndawatsitsa ndi 15 Ali Ku
Manyumba imodzi ndi ya Zidina zowotcha atatuwa ndizosawotcha ,size ya plot ndi 20 by 40 meters Manyumbawa Ali mseu wopita Ku area 49 Dubai Madzi ndi magetsi zili pafupi Phone yanga ndi :0992335517