Ndatsitsiratu manyumbawa ali ku area 50 lilongwe alipo okwana 4

Manyumbawa ali mseu wopita ku area 49 Dubai Pali manyumba okwana 4 ali pamalo amodzi ,imodzi ili ndi zidina zowotcha chilichonse mkati anamaliza ngakhale wiring inapangidwa kale Madzi ndi magetsi zili pafupi Ndatsitsa ndi 15% amene apange changu ndidzamuchotseranso Phone yanga ndi :0992335517

FREE

seller's name'
Name: Mwendothamanga P
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 11 January, 2022

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0992335517

Product Images

product image 0
Image 1 of 3
product image 1
Image 2 of 3
product image 2
Image 3 of 3