Manyumba yogulitsa ndatsitsa ndi 30 pali manyumba okwana 4 ali
Pali manyumba okwana 4 ali pa plot imodzi ndipo ali mseu wopita ku area 49 Dubai madzi ndi magetsi zilipafupi Plot size ndi 20 by 40 meters Phone yanga : 0992335517 Ili ku area 50 lilongwe