Manyumba okwana 4 akugulitsidwa ali pamalo amodzi size ya plot

Ma plot atsala atatu basi azanu akuguliratu chifukwa ndatsitsiratu mtengo. Mwezi wogula Malo ndi mwezi womwe uno wamawa tiyamba kukweza ndiye ndi bwino kugula mudzi wonse ndi ndalama yochepa . Mutagula ndalama yanu iyamba mubwera chifukwa pali makomo six plus imene akunkhala eni wake Malo ndi business yosaluza mutagula Malo mwapanga mtsogolo Ngati muli ndi mafunso kapena mukufuna akundziwa zambiri ndiyimbireni pa phone number:0992335517

FREE

seller's name'
Name: Chingwalungwalu M
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 01 February, 2022

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0992335517

Product Images

product image 0
Image 1 of 3
product image 1
Image 2 of 3
product image 2
Image 3 of 3
Loading recommendations...