Manyumba ogulitsa alipo okwana 4 ali pa plot imodzi ndikugulitsa
Manyumbawa ali mseu wopita ku area 49 Dubai Madzi ndi magetsi zili pafupi kwambiri Ngati muli ndi mafunso kapena mukufuna akundziwa zambiri chonde ndiyimbireni pa phone number yanga iyi:0992335517/0885837201