Malo Ogulitsa Ku Lilongwe Area 24 Katondo Ndi akulu 45 by 50 Ali mphepete mwa nseu waukulu omwe ufuna kuthilidwa phula Madzi ndi magetsi zil pafupi kwambil Ndi a flat Ama bussiness mukhoza kumangapo ma shop kaya School kaya Lodge even ma mansion atatu akhoza kuyimapo Ndiimbilen pa 0997050324 WhatsAap 0882889992 Chidziwitso Palibepo Agent aliyese muzakumana ndi munu wake straight Mtengo oyambila ndi 8 million
$8