Tiri ndi farm yogulitsa ku mselema m'boma la machinga farm iyi Ili Malo abwino Pali nyumba za ma 2 bedrooms nyumbazi ziripo zokwana 16 ndiye Pali nyumba imodzi ya 4 bedrooms sitting room dining kitchen stores ceiling paliso sweeming pool pump ya mafuta agalimoto thank yosungira madzi mjingo msinje isatha madzi mitengo ya chilengedwe tractor imodzi ma balan chinyumba chosungira katundu Ware house office kukula kwake ndi 176 hectors magesi Ali pafupi mtengo ndi 230 million kukambirana imban pa manambala awa 0995917669/0884098591
FREE