Pezani Smartphone pangongole , nthawi yoma user ma phone ochotsa battery inatha .. panopa tili ndi SPARK 8 komaso TECNO pop 5 , ngongoleyi ndi ya wina aliyese ndipo umabweza kwa chaka chimodzi , tipezeni ku shop yathu mu mzinda wa Lilongwe ,pa depot ya magalimoto opita ku 25 moyang'anizana ndi depot ya kachikunkhu, Shop yathu inalembedwa kuti MOBILE KINGZ , akutali mutha kutipeza pa ma number awa ndipo muzathandizidwa:
$38