Plot ya k800 000 ija ndi imeneyi. Ili ku area 51 kwa Nzumazi. Mukalowa pa bridge ya 51 kukwezeka mtunda kudusa pachigayo chapa mtaba. Muzakhota pa 4 ways yomwe pali 'mortuary' kumalowera nsewu opita ku Rugby stadium. Malowa ali moyang'anizana ndi nsewu opita ku chipatala. Kukula kwake ndi 15 by 30. Anthu ndithu akumanga kumenek. Call/Whatsapp+265888052362
MK1