KO'd mukungokhala kapena muli ndi mpamba ochepa mukusowa poyambira. Ifetu timaphunzitsa anthu kapangidwe ka samoosa ,mandasi,zitumbuwa,zisope,ma skone ,cup cake,vanilla birthday cake ,cake decoration zonsezi pamtengo 550 basi anzanu anaphunzira pano analembaso aganyu akuwagulitsira ma bzness awo misikamu zikutheka ndithu nanu tipezeni pa 0992530979 kuti muphunzire nawo
$550