Peoples. Ndili ndi malo Ku Karonga omwe ndimafuna kumangapo Cottage along the lake. Malowa ali position yabwino kwambiri for accommodation business. Or a retirement dream house. Tinayambakoso kale kuwakonza ready for building . madzi & magetsi alipo.
FREE