Machine wa amagaya nyama komanso mutha kugwiritsa ntchito popanga sausage ,mukagura machine wa muzaphunziranso kupanga sausage yamitindu iwiri mwa ulele komanso sipokhapo muzalandira pdf yoku thandizirani kupangani guide panthawi imene muku panga sausage.
$35