Plot yogulitsa pa Madisi kuseli kwa Kanjiwa filling Station, pali nyumba 5. Madzi komaso magetsi alipo. Mtengo ukuyamba ndi 7.5million koma kukambirana kulipo. Mungathe kuimba pa 0999559297 kuti mudziwe zambiri.
FREE