Nyumbayi ili ndi three bedroom, sitting room, dining room, kitchen, stores, two bathroom, two toilet Size yanyumba ndi 8 by 30 meters Mtengo ndi wokambirana Nyumbayi ili pafupi ndi praise private school Ngati mwayikonda nyumbayi kuti mukamalizitsa nonkha tiyeni tikambirane pondiyimbira phone number yanga ndi:0992335517/0885837201
FREE