Plot yogulitsa ku Area 56 Mtandire near Roman Catholic Kamkodola

Plot yaikulu. Kuli main house komanso nyumba zina za rent komanso mashop awiri olumikizana ndi mpanda kutsogolo. Ku mpanda komanso nyumba zonse zamagesi. Ndalama zonse za rent zomwe zimatoleledwa pamwezi ndi 135,000 kupatula nyumba yaikulu yomwe amakhala enuwake koma kupangitsa rent itha kukhala 70 to 80 thousands. Mtengo omwe tikufunapo ndi 7.5 million. Lilongwe 0999809730/0884552255.

FREE

seller's name'
Name: Samson K
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 03 September, 2022

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 5
product image 1
Image 2 of 5
product image 2
Image 3 of 5
product image 3
Image 4 of 5
product image 4
Image 5 of 5