Nyumba yogulitsa ku area 50 lilongwe ili ndi makomo awiri
Kuchoka mu tala kufika pa malowa ndi ma plot atatu mwafika pa plot Madzi ndi magetsi ali pafupi kwambiri Mtengo ndi 8.7 million kukambirana kulipo Phone number yanga ndi iyi:0992335517/0885837201