Tikuyambapo our ONLINE SEWING CLASSES pa 27 November pano. Tiyeni tiphunzire limodzi, luso lamanja siliguga! Ndi K12,000 yokha pa mwezi. Pay a deposit to reserve your spot. (We also have malo angapo ku weekday ndi weekend classes). 0997839897. ~Mwinjiro
MK12,000