ELECTRONIC OVERLOCK SEWING MACHINES

Matelala amzathu zatengeni machine awa a overlock amagetsi. Machine mbambande opanda madando oti kutenga mkuyamba kugwiritsa ntchito. Machine oti kusokera zovala kumaoneka cha original. Amzathu omwe mumapanga business yogula ndikubweza zovala deal ndi imeneyi. Mutha kuchepetsa size yazovala ndi kusokera overlock kumaoneka ngati za original chifukwa cha overlock. Zipangizo zake zonse zilipo ndithu.

$135

seller's name'
Name: Mphawi N
seller phone number
Location: Blantyre
uploaded on
Date: 04 December, 2022

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4