Malo ogulitsa alipo ku Lunzu Gada Bt Plot ndi mk 500 pin kma nzotheka kuphatikiza Mwayi olipila pangono pangono ulipo. Kuchoka mu tarmac ndi ulendo oyendeka ndithu Tipezen poimba +265992710149 / 0888704445
$491