Amzathu wogulitsa nyama, eni ma shop, restaurant, hotels, bottlestores, wogulitsa ma soft drinks ndi ena nonse. Katundu mumamfuna uja ndameneyu. Fridge iyi sidakonzedwepo kapena kuthiridwa gas, original paint. imaumitsa kathithi ndipo imalira 24/7. No agents are involved.
$800