Malata openta kale pa mtengo okambilana,tili ndi ma type ose amalata komaso ma size ose kuyambira 1 feet mpaka pothela nyumba yanu,ma customer athu akutali ndi mzinda wa Lilongwe musadele nkhawa timatumiza pa mtengo wa bwino mwachitsazo ku Zomba mukatigula malata 40 mudzalipila 20,000 basi,tipezeni ku Lilongwe komwe amagulitsilako matabwa or timbileni pa 0993242921
$12