Kuli nyumba ziwiri, main house komanso semi-detached tenants house. Ku mpanda kwa gate komanso space yaikulu komanso garden. Kuli madzi a water board komanso chitsime. Magesi asanalowe koma ma electric lines aliko kale komanso transformer ya Escom ili pafupi. Plot yabwino kwambiri with good neighborhood. Zambiri muzadzionera nokha pomwepo ife tikungofunapo 8.5 million basi kumvananso kulipo. Zativuta ndife. Lilongwe 0999809730.
FREE