Malo ogulisa ku Lilongwe, Area 36 . Pali nyumba ziwiri, imodzi yamakomo atatu yamagetsi kale Ina yayikulu yamagetsi nso. Palinso ka unfinished shop pompo with space plenty space aside. Hit inbox or call/Wap 0888760952
MK10,000,000