Malo ogulisa BT kwa mkoka pafupi ndi graund yapa mkoka

Kwa ofuna kugula ku nancholi BT kwa mkoka pafupi ndi graund yapa mkoka ntengo ndi 1.5 nzokambilana muka bwela kudza ona kumvana kulipo osati zomango yesa ndati kwa ofuna kugula okha msewu madzi magesi zonse zili pafupi

MK1

seller's name'
Name: Tiya S
seller phone number
Location: Blantyre
uploaded on
Date: 08 May, 2023

Contact Seller

Product Images

product image 0
Image 1 of 2
product image 1
Image 2 of 2