Nyumba ziwiri ku Namiyango Bangwe zakumpanda zasika mtengo kuchokera PA 28 million kufika PA 26 million komaso kukambirana kulipo. Zonse ndi za safe contained madzi magesi zilipo Kale 0888336644
$26