Zilibe agent izi-dzatengeni katunduyi muyambe kulandira za rent pompopompo! Nyumba 5 zamagetsi, ziwiri ndiza self contained plan _zili mumpanda car park ilipo, palinso shop imodzi yaikulu bwino kwa inu okonda geni!Msewu ulipo wabwino zedi, mpope ulipo kale.Plaster+cement floor zinapangidwa mkati mwa nyumba zonse.Inu tabwerani timvanepo apa(26mln-_nego)...ndili ku area 36pafupi ndi Favoured pvt school.Palinso keep thekera kowadula pakati malowa_dzaoneni nokha.0995292771/0888740184(Wap).
$26,000,000