Ndalama zisamangokhala,yambani business ya nyumba za rent! Nyumba 5 zamagetsi (ziwiri zazikulu za self contained plan+zitatu ma quarters amakomo awiri iliyonse.Gulani zonse pa 27million! Magetsi akuyaka makomo onse, mpope+mpanda wa njerwa zilipo.Palinso shop imodzi yaikulu bwino.Ndilankhuleni Ine mwini wake(area36_pafupi ndi Favoured pvt school). pa0995292771/0888740184(WhatsApp)timvanepo ife tupita kukakhala kumudzi.Monse muli a rent,mukagula-zanu zikuyamba kubweza pompopompo! Don't just go for quality, rather go for value!
$28,000,000