MALO MUNDA

Munda ogulitsa kwa Mpingu pafupi ndi Chaminade Secondary school. Mutha kumalimapo kapena kumangapo makola. Magetsi ali pafupi, yatsala 2 acres. K650,000 per acre. Kukambilanaso kulipo.

$650

seller's name'
Name: Hamisi Z
seller phone number
Location: Lilongwe
uploaded on
Date: 19 May, 2023

Contact Seller