IRON KINGS malata, ndi company yomwe ikupanga komaso kugulitsa malata pa mtengo otsika kwambiri, tili ndi ma type ose amalata monga IBR CORRUGATED NDI VERSATILE, ma Ridge ma valley misomali wire zosezo tili nazo tipezeni ku factory shop yathu moyandikana ndi msika wa matabwa mtwn ya Lilongwe, kwa ma customer athu akutali ingotiuzani type ndi color yomwe mukufuna ifeyo tidzabweletsa kwanu konko ndalama mudzapeleka katundu wanu atafika timbileni pa 0993242921
$12