Ndikupeze ndi ufa wa bwino wangopangidwa kumene ku factory 5kgs K4500 10kgs K9500 25kgs K22500 50kgs K54000 Ndiliso ndi ma maize grits grade 2ma 50Kgs ndiyakhuleni pa 0991187850 ndikupezeka mkanengo ndiyakhuleni timvane bho bho
MK4,500