Mukuchedwa pati!? Nyumba izi 5 ku area36(pafupi ndi Favoured pvt school) kumpanda zonse zamagetsi.Mkati zinapangidwa kale plaster+cement floor_zangotsala ma finishing.Ma agent mukhoza kubwera ndi buyer.Price 23million_negotiable. Nyumba zazikulu zilipo zitatu(ziwiri ndiza self contained plan),pali ma quarters awiri+ shop.Mpope ulipo & plot ili pamsewu wabwino.Pamwezi za rent amount timapeza 335pin.Musaphonye mwayiwu,imbani 0995292771/Whatsapp 0888740184.
$23,000,000