Mmawa wabwino kwa inu nonse ma customer. Tikupezeka ndi ma LED TV pa mitengo yotsika, ma TV wa ali picture a quality komanso ndi olimba. Pali ma sizes ngati 30 inches mpaka 60". Tipezeni mu Town ya Lilongwe, ku devil Street. Dziwani mitengo yathu 30" LED TV Mk 135,000 32" LED TV MK 165,000 42" LED TV Mk 260,000 42" SMART TV Mk 350,000 50" LED TV MK 400,000 50" SMART TV MK 470,000 55" SMART TV MK 550,000 60" SMART TV MK 650,000
MK170,000