House in salima

Nyumba yaikulu kuseluku kuliso Malo okwana nyumba ngati yomweyi. Ndikofika galimoto nyumba ya zipinda 4 plus stores, dinning room, comfortable sitting room, mawindo azitsulo. Malo a phee osathithikana madzi a water board ali pafupi magesi about 300 metres from pali pholo. Mukafuna kuziwa zambiri imbani pa 0990380048 or Whatsapp on 0881748217. Mtengo ndi 5.5 million salima kaphatenga! Ku kambiranaso kulipo gwiritsani ntchito ndalama yanu molondola pogula chinthu cholozeka come and see the house for yourself and for discount contact me now.

$5

seller's name'
Name: Cuthbert V
seller phone number
Location: Blantyre
uploaded on
Date: 18 June, 2023

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0990380048
seller phone number Phone Number: 0881748217

Product Images

product image 0
Image 1 of 3
product image 1
Image 2 of 3
product image 2
Image 3 of 3