NGATI MWAKHALA MUKUFUNA KUGULA NYUMBA YABWINO NDI MALO ABWINO KOMANSO DERA LABWINO, BWERANI TSOPANO MUGULE NYUMBA IYI KUNO KWA BVUMBWE, NDIPO ZONSE ZOYENERA ZILIPO, NYUMBA YABWINO,MALO ABWINO MOTI PALINSO NTHOCHI, MITENGO YAZIPASO YOPATSA CHIDWI KWAMBIRI.
$350,000