Plots on sale

Kupeza plot kwamphweka!!!!!!!!! Ndi BNG INVESTMENT mutha kupeza plot polipira pang'ono pang'ono kwa miyezi 12 ma plot wa Ali ku area 54 moyang'anizana ndi international airport ndipo mtengo ndi 950,000 cash komaso 1,200,000 kupeleka miyezi 12 size nd 15 by 30 ndipo mapelekedwe Ake nd 100,000 mwezi uliwose mpaka miyezi 12 ngooooo zabwino zipose APA? See more

MK950,000

seller's name'
Name: Çútë Ñ
seller phone number
Location: Kawale 2, Lilongwe
uploaded on
Date: 03 July, 2023

Contact Seller