Sitingamadalire madzi a waterboard nthawi zonse, pali ntchito zina zofuna madzi a pa Chitsime monga, gardening, car washing, bathing and toilet flushing or kumwa kumene iyaa. Ife ntchito zathu ndi zokumba zitsime komanso kuikira ma pump a madzi. Ku Golomoti, ku Lumbadzi, ku Mzimba ndi madela ena ntchito zikupitilira. Timakumba zitsime mwamakono See more
FREE