Nyumba yogulitsa ku Blantyre kulunzu kukula

Nyumba yogulitsa ku Blantyre kulunzu,mbairi mwa msewu, malowa ali pabwino ok, 1 Pali nyumba 4 za rend, 2 madzi Alipo, 3 magesi alipo, 4 msewu ulipo, 5 kumpanda komanso ku space yaikuru mutha kikako nyumba ziwiri, 6 pari ma barber shop atatu ndi shop, Pamwezi timatolara 266 thousand kwacha. Mtengo woyambila ndi 45 million kwacha, kukambilanananso kulipo. Numbers 0999111635 call or Whatsapp, 0888651347 call only. Malo ake ndi awa

FREE

seller's name'
Name: Josephy B
seller phone number
Location: Blantyre
uploaded on
Date: 23 July, 2023

Contact Seller

seller phone number Phone Number: 0999111635
seller phone number Phone Number: 0888651347

Product Images

product image 0
Image 1 of 4
product image 1
Image 2 of 4
product image 2
Image 3 of 4
product image 3
Image 4 of 4